31 Ine ndamva mawu angati a mkazi amene akumva ululu,
Ndamva ngati kubuula kwa mkazi amene akubereka mwana wake woyamba,
Koma ndi mawu a mwana wamkazi wa Ziyoni amene akupuma movutikira.
Iye akutambasula manja ake nʼkunena kuti:+
“Mayo ine, ndatopa ndi anthu amene akufuna kundipha!”