Yeremiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mumtima mwawo sanena kuti: “Tiyeni tsopano tiope Yehova Mulungu wathu,Amene amatigwetsera mvula mʼnyengo yake,Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira,Amene amaonetsetsa kuti tikukolola pa nthawi yake.”*+
24 Mumtima mwawo sanena kuti: “Tiyeni tsopano tiope Yehova Mulungu wathu,Amene amatigwetsera mvula mʼnyengo yake,Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira,Amene amaonetsetsa kuti tikukolola pa nthawi yake.”*+