Yeremiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bisalani inu ana a Benjamini, thawani mu Yerusalemu. Imbani lipenga la nyanga+ ya nkhosa ku Tekowa.+Yatsani chizindikiro cha moto ku Beti-hakeremu, Chifukwa tsoka likubwera kuchokera kumpoto ndipo ndi lalikulu kwambiri.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 14
6 Bisalani inu ana a Benjamini, thawani mu Yerusalemu. Imbani lipenga la nyanga+ ya nkhosa ku Tekowa.+Yatsani chizindikiro cha moto ku Beti-hakeremu, Chifukwa tsoka likubwera kuchokera kumpoto ndipo ndi lalikulu kwambiri.+