Yeremiya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Dulani mitengo kuti timange malo okwera oti timenyerepo nkhondo ndi Yerusalemu.+ Yerusalemu ndi mzinda umene ukuyenera kuimbidwa mlandu.Mkati mwake muli kuponderezana kokhakokha.+
6 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Dulani mitengo kuti timange malo okwera oti timenyerepo nkhondo ndi Yerusalemu.+ Yerusalemu ndi mzinda umene ukuyenera kuimbidwa mlandu.Mkati mwake muli kuponderezana kokhakokha.+