Yeremiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mofanana ndi chitsime chimene chimatulutsa madzi ozizira,Yerusalemu amatulutsanso zinthu zoipa. Mkati mwake mukumveka phokoso la chiwawa komanso kuponderezana.+Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.
7 Mofanana ndi chitsime chimene chimatulutsa madzi ozizira,Yerusalemu amatulutsanso zinthu zoipa. Mkati mwake mukumveka phokoso la chiwawa komanso kuponderezana.+Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.