-
Yeremiya 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:
“Adani adzakunkha otsalira onse a Isiraeli ngati mmene amakunkhira mphesa zomaliza pa mtengo wa mpesa.
Kwezanso dzanja lako ngati munthu amene akuthyola mphesa panthambi za mtengo wa mpesa.”
-