Yeremiya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi ndilankhule ndi ndani nʼkumuchenjeza? Ndi ndani adzamvetsere? Taonani! Makutu awo ndi otseka,* choncho sangathe kumva.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala chinthu chimene akunyansidwa nacho+Ndipo sakusangalala nawo. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:10 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 18
10 “Kodi ndilankhule ndi ndani nʼkumuchenjeza? Ndi ndani adzamvetsere? Taonani! Makutu awo ndi otseka,* choncho sangathe kumva.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala chinthu chimene akunyansidwa nacho+Ndipo sakusangalala nawo.