Yeremiya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chifukwa aliyense kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, akupeza phindu mwachinyengo.+Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense akuchita zachinyengo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, ptsa. 11-12
13 “Chifukwa aliyense kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, akupeza phindu mwachinyengo.+Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense akuchita zachinyengo.+