Yeremiya 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,Ndipo iwo adzapunthwa ndi zinthu zimenezi,Abambo limodzi ndi ana,Munthu ndi mnzake woyandikana naye,Onse adzawonongedwa.”+
21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,Ndipo iwo adzapunthwa ndi zinthu zimenezi,Abambo limodzi ndi ana,Munthu ndi mnzake woyandikana naye,Onse adzawonongedwa.”+