Yeremiya 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga,Vala chiguduli+ ndipo ugubuduke mʼphulusa. Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo, ulire mowawidwa mtima,+Chifukwa wowononga adzatiukira modzidzimutsa.+
26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga,Vala chiguduli+ ndipo ugubuduke mʼphulusa. Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo, ulire mowawidwa mtima,+Chifukwa wowononga adzatiukira modzidzimutsa.+