Yeremiya 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ngati simudzapondereza alendo okhala pakati panu, ana amasiye ndi akazi amasiye,+ komanso ngati simudzakhetsa magazi a munthu wosalakwa mʼdziko lino ndiponso ngati simudzatsatira milungu ina, zimene zingakubweretsereni mavuto,+
6 ngati simudzapondereza alendo okhala pakati panu, ana amasiye ndi akazi amasiye,+ komanso ngati simudzakhetsa magazi a munthu wosalakwa mʼdziko lino ndiponso ngati simudzatsatira milungu ina, zimene zingakubweretsereni mavuto,+