Yeremiya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho nyumba imene ikudziwika ndi dzina langa,+ imene mukuidalira+ ndiponso pamalo awa amene ndinawapereka kwa inu ndi makolo anu, ndidzachita zofanana ndi zimene ndinachita ku Silo.+
14 Choncho nyumba imene ikudziwika ndi dzina langa,+ imene mukuidalira+ ndiponso pamalo awa amene ndinawapereka kwa inu ndi makolo anu, ndidzachita zofanana ndi zimene ndinachita ku Silo.+