Yeremiya 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Koma kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ akutero Yehova. ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha nʼkudzichititsa manyazi?’+
19 ‘Koma kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ akutero Yehova. ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha nʼkudzichititsa manyazi?’+