Yeremiya 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwatu pa tsiku limene ndinatulutsa makolo anu mʼdziko la Iguputo, sindinalankhule nawo chilichonse kapena kuwalamula zokhudza kupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.+
22 Chifukwatu pa tsiku limene ndinatulutsa makolo anu mʼdziko la Iguputo, sindinalankhule nawo chilichonse kapena kuwalamula zokhudza kupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.+