Yeremiya 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka mʼdziko la Iguputo mpaka pano.+ Choncho ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse omwe ndi aneneri, ndinkawatumiza tsiku lililonse, mobwerezabwereza.*+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Nsanja ya Olonda,2/15/1993, tsa. 324/1/1988, tsa. 22
25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka mʼdziko la Iguputo mpaka pano.+ Choncho ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse omwe ndi aneneri, ndinkawatumiza tsiku lililonse, mobwerezabwereza.*+