Yeremiya 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo udzawauze kuti, ‘Uwu ndi mtundu wa anthu umene sunamvere mawu a Yehova Mulungu wawo, ndipo anakana kulandira malangizo.* Palibe munthu wokhulupirika pakati pawo ndipo satchulanso nʼkomwe za kukhulupirika.’*+
28 Ndipo udzawauze kuti, ‘Uwu ndi mtundu wa anthu umene sunamvere mawu a Yehova Mulungu wawo, ndipo anakana kulandira malangizo.* Palibe munthu wokhulupirika pakati pawo ndipo satchulanso nʼkomwe za kukhulupirika.’*+