Yeremiya 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Meta tsitsi lako lalitalilo* nʼkulitaya ndipo ukwere pamapiri opanda mitengo nʼkukaimba nyimbo yoimba polira, chifukwa Yehova wakana ndiponso wasiya mʼbadwo uwu umene wamukwiyitsa.
29 Meta tsitsi lako lalitalilo* nʼkulitaya ndipo ukwere pamapiri opanda mitengo nʼkukaimba nyimbo yoimba polira, chifukwa Yehova wakana ndiponso wasiya mʼbadwo uwu umene wamukwiyitsa.