Yeremiya 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Chifukwa mbadwa za Yuda zachita zinthu zoipa mʼmaso mwanga,’ akutero Yehova. ‘Aika mafano awo onyansa mʼnyumba imene imadziwika ndi dzina langa nʼcholinga choti aidetse.+
30 ‘Chifukwa mbadwa za Yuda zachita zinthu zoipa mʼmaso mwanga,’ akutero Yehova. ‘Aika mafano awo onyansa mʼnyumba imene imadziwika ndi dzina langa nʼcholinga choti aidetse.+