2 Mafupawo adzamwazidwa padzuwa, pamwezi ndi panyenyezi zonse zakumwamba zimene ankazikonda, kuzitumikira, kuzitsatira, kuzifunafuna ndi kuzigwadira.+ Anthu sadzasonkhanitsa mafupawo pamodzi nʼkuwaika mʼmanda ndipo adzakhala ngati manyowa panthaka.”+