Yeremiya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chiyani anthu awa, anthu okhala mu Yerusalemu, ali osakhulupirika ndipo akhalabe osakhulupirika kwa nthawi yaitali chonchi? Iwo akupitiriza kuchita zachinyengoNdipo akukana kubwerera.+
5 Nʼchifukwa chiyani anthu awa, anthu okhala mu Yerusalemu, ali osakhulupirika ndipo akhalabe osakhulupirika kwa nthawi yaitali chonchi? Iwo akupitiriza kuchita zachinyengoNdipo akukana kubwerera.+