-
Yeremiya 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ine ndinatchera khutu ndipo ndinapitiriza kuwamvetsera. Koma zimene iwo ankanena sizinali zoona.
Panalibe munthu amene analapa zoipa zimene ankachita, kapena amene anafunsa kuti, ‘Nʼchiyani chimene ndachitachi?’+
Aliyense akungobwerera kunjira imene anthu ambiri akuitsatira, ngati hatchi imene ikuthamangira kunkhondo.
-