Yeremiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale dokowe, mbalame youluka mumlengalenga, imadziwa bwino nthawi yake yoikidwiratu.Ndipo njiwa, namzeze komanso mbalame zina, zimadziwa nthawi yobwerera kumene zachokera.* Koma anthu anga sakudziwa chiweruzo cha Yehova.”’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 17 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 6 2016, tsatsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,8/1/2002, tsa. 32
7 Ngakhale dokowe, mbalame youluka mumlengalenga, imadziwa bwino nthawi yake yoikidwiratu.Ndipo njiwa, namzeze komanso mbalame zina, zimadziwa nthawi yobwerera kumene zachokera.* Koma anthu anga sakudziwa chiweruzo cha Yehova.”’+
8:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 17 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 6 2016, tsatsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,8/1/2002, tsa. 32