Yeremiya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu anzeru achititsidwa manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova.Ndipo kodi ali ndi nzeru zotani?
9 Anthu anzeru achititsidwa manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova.Ndipo kodi ali ndi nzeru zotani?