Yeremiya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho akazi awo ndidzawapereka kwa amuna ena,Minda yawo ndidzaipereka kwa anthu ena.+Chifukwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, aliyense akupeza phindu mwachinyengo.+Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense akuchita zachinyengo.+
10 Choncho akazi awo ndidzawapereka kwa amuna ena,Minda yawo ndidzaipereka kwa anthu ena.+Chifukwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, aliyense akupeza phindu mwachinyengo.+Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense akuchita zachinyengo.+