Yeremiya 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo kuwonongeka kwa mwana wamkazi* wa anthu anga ponena kuti,‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ Pamene kulibe mtendere.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 1210/1/1986, tsa. 30
11 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo kuwonongeka kwa mwana wamkazi* wa anthu anga ponena kuti,‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ Pamene kulibe mtendere.+