-
Yeremiya 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 “‘Ndikadzawasonkhanitsa, ndidzawawononga,’ akutero Yehova.
‘Mumtengo wa mpesa simudzapezeka mphesa zotsala, mumtengo wa mkuyu simudzapezeka nkhuyu ndipo masamba adzafota.
Zinthu zimene ndinawapatsa zidzatayika.’”
-