Yeremiya 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mahatchi ake akumveka kupuma mwawefuwefu ali ku Dani. Dziko lonse lagwedezekaChifukwa cha phokoso la kumemesa* kwa mahatchi ake amphongo. Adani akubwera kudzawononga dziko ndi chilichonse chimene chili mmenemo,Mzinda ndi anthu okhala mmenemo.”
16 Mahatchi ake akumveka kupuma mwawefuwefu ali ku Dani. Dziko lonse lagwedezekaChifukwa cha phokoso la kumemesa* kwa mahatchi ake amphongo. Adani akubwera kudzawononga dziko ndi chilichonse chimene chili mmenemo,Mzinda ndi anthu okhala mmenemo.”