-
Yeremiya 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Ine ndikutumiza njoka pakati panu,
Njoka zapoizoni zimene simungazinyengerere kuti muziseweretse,
Ndipo zidzakulumani ndithu,” akutero Yehova.
-