-
Yeremiya 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pakumveka mawu olirira thandizo kuchokera kudziko lakutali,
Kuchokera kwa mwana wamkazi wa anthu anga.
Iye akuti: “Kodi Yehova sali mu Ziyoni?
Kapena kodi mfumu yake mulibe mmenemo?”
“Nʼchifukwa chiyani andikhumudwitsa ndi mafano awo ogoba,
Ndiponso milungu yawo yachilendo yopanda pake?”
-