Yeremiya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:22 Nsanja ya Olonda,6/1/2010, ptsa. 21-22 Yeremiya, tsa. 135
22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+