Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda mʼmutu mwanga mukanakhala madzi ambiri,Ndiponso maso anga akanakhala kasupe wa misozi.+ Zikanatero, ndikanalira masana ndi usikuChifukwa cha anthu a mtundu wanga amene aphedwa.
9 Ndikanakonda mʼmutu mwanga mukanakhala madzi ambiri,Ndiponso maso anga akanakhala kasupe wa misozi.+ Zikanatero, ndikanalira masana ndi usikuChifukwa cha anthu a mtundu wanga amene aphedwa.