Yeremiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikanakonda ndikanakhala ndi malo ogona anthu apaulendo mʼchipululu. Zikanatero, ndikanasiya anthu a mtundu wanga nʼkuwachokera,Chifukwa onse ndi achigololo,+Gulu la anthu ochita zachinyengo.
2 Ndikanakonda ndikanakhala ndi malo ogona anthu apaulendo mʼchipululu. Zikanatero, ndikanasiya anthu a mtundu wanga nʼkuwachokera,Chifukwa onse ndi achigololo,+Gulu la anthu ochita zachinyengo.