Yeremiya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ndi okonzeka kunama ngati uta umene wakungidwa.Dzikolo ladzaza ndi chinyengo ndipo palibe amene ali wokhulupirika.+ “Iwo akuchita zoipa motsatizanatsatizana,Ndipo akundinyalanyaza,”+ akutero Yehova.
3 Iwo ndi okonzeka kunama ngati uta umene wakungidwa.Dzikolo ladzaza ndi chinyengo ndipo palibe amene ali wokhulupirika.+ “Iwo akuchita zoipa motsatizanatsatizana,Ndipo akundinyalanyaza,”+ akutero Yehova.