Yeremiya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense amapusitsa mnzake,Ndipo palibe amene amalankhula zoona. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo amadzitopetsa okha pochita zinthu zoipa.
5 Aliyense amapusitsa mnzake,Ndipo palibe amene amalankhula zoona. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo amadzitopetsa okha pochita zinthu zoipa.