-
Yeremiya 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Lilime lawo ndi muvi wakupha umene umalankhula zachinyengo.
Munthu amalankhula mwamtendere ndi mnzake,
Koma mumtima mwake amakonza chiwembu.”
-