Yeremiya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi sindikuyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” akutero Yehova. “Kodi sindikuyenera kubwezera mtundu wa anthu oterewa?+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 26
9 “Kodi sindikuyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” akutero Yehova. “Kodi sindikuyenera kubwezera mtundu wa anthu oterewa?+