Yeremiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+
11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+