-
Yeremiya 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kodi wanzeru ndi ndani kuti amvetse zimenezi,
Kodi Yehova walankhula ndi ndani kuti anene zimenezi?
Nʼchifukwa chiyani dzikoli lawonongedwa?
Nʼchifukwa chiyani lawotchedwa nʼkukhala ngati chipululu
Chimene palibe munthu amene akudutsamo?”
-