Yeremiya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼmalo mwake, anatsatira zofuna za mitima yawo mouma khosi+ ndipo anatsatira mafano a Baala, mogwirizana ndi zimene makolo awo anawaphunzitsa.+
14 Mʼmalo mwake, anatsatira zofuna za mitima yawo mouma khosi+ ndipo anatsatira mafano a Baala, mogwirizana ndi zimene makolo awo anawaphunzitsa.+