Yeremiya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+
15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+