Yeremiya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa ku Ziyoni kwamveka anthu akulira mofuula kuti:+ “Tawonongedwa kwambiri! Tachita manyazi kwambiri! Chifukwa tasiya dziko lathu ndipo atigwetsera nyumba zathu.”+
19 Chifukwa ku Ziyoni kwamveka anthu akulira mofuula kuti:+ “Tawonongedwa kwambiri! Tachita manyazi kwambiri! Chifukwa tasiya dziko lathu ndipo atigwetsera nyumba zathu.”+