Yeremiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Akazi inu, tamverani mawu a Yehova. Tcherani khutu kuti mumve mawu otuluka mʼkamwa mwake. Phunzitsani ana anu aakazi kulira maliroNdipo aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polirayi.+
20 Akazi inu, tamverani mawu a Yehova. Tcherani khutu kuti mumve mawu otuluka mʼkamwa mwake. Phunzitsani ana anu aakazi kulira maliroNdipo aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polirayi.+