Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa imfa yatilowera mʼnyumba kudzera mʼmawindo.Yalowa munsanja zathu zokhala ndi makoma olimbaKuti mumsewu musapezeke mwana aliyenseNdiponso kuti anyamata asapezeke mʼmabwalo a mzinda.’+
21 Chifukwa imfa yatilowera mʼnyumba kudzera mʼmawindo.Yalowa munsanja zathu zokhala ndi makoma olimbaKuti mumsewu musapezeke mwana aliyenseNdiponso kuti anyamata asapezeke mʼmabwalo a mzinda.’+