Yeremiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mitembo ya anthu idzangoti mbwee panthaka ngati manyowa.Idzakhala ngati tirigu amene angomumweta kumeneKoma popanda munthu womusonkhanitsa pamodzi.”’”+
22 Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mitembo ya anthu idzangoti mbwee panthaka ngati manyowa.Idzakhala ngati tirigu amene angomumweta kumeneKoma popanda munthu womusonkhanitsa pamodzi.”’”+