Yeremiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitame chifukwa cha nzeru zake.+Munthu wamphamvu asadzitame chifukwa cha mphamvu zake.Ndipo munthu wachuma asadzitame chifukwa cha chuma chake.”+
23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitame chifukwa cha nzeru zake.+Munthu wamphamvu asadzitame chifukwa cha mphamvu zake.Ndipo munthu wachuma asadzitame chifukwa cha chuma chake.”+