26 Ndidzaimba mlandu Iguputo,+ Yuda,+ Edomu,+ Aamoni+ ndi Mowabu+ komanso onse odulira ndevu zawo zamʼmbali amene amakhala mʼchipululu.+ Chifukwa mitundu yonse ndi yosadulidwa ndipo anthu onse a mʼnyumba ya Isiraeli sanachite mdulidwe wa mitima yawo.”+