Yeremiya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse ndi opanda nzeru ndiponso opusa.+ Malangizo ochokera pamtengo amalimbikitsa anthu kuchita zachabechabe.+
8 Onse ndi opanda nzeru ndiponso opusa.+ Malangizo ochokera pamtengo amalimbikitsa anthu kuchita zachabechabe.+