Yeremiya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo ndi achabechabe, oyenera kunyozedwa.+ Tsiku loti aweruzidwe likadzafika adzawonongedwa.