Yeremiya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tenti yanga yawonongedwa ndipo zingwe zanga zonse zomangira tentiyo aziduladula.+ Ana anga aamuna andisiya ndipo kulibenso.+ Palibe aliyense amene watsala woti atambasule tenti yanga kapena kudzutsa nsalu za tentiyo.
20 Tenti yanga yawonongedwa ndipo zingwe zanga zonse zomangira tentiyo aziduladula.+ Ana anga aamuna andisiya ndipo kulibenso.+ Palibe aliyense amene watsala woti atambasule tenti yanga kapena kudzutsa nsalu za tentiyo.