Yeremiya 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Komanso pa mafuko amene saitana pa dzina lanu. Chifukwa iwo awononga mbadwa zonse za Yakobo,+Amuwononga mpaka kufika potheratu,+Ndipo dziko lake alisandutsa bwinja.+
25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Komanso pa mafuko amene saitana pa dzina lanu. Chifukwa iwo awononga mbadwa zonse za Yakobo,+Amuwononga mpaka kufika potheratu,+Ndipo dziko lake alisandutsa bwinja.+